Mamasulidwe a kwa Omangidwa (Liberty to the Captives)
Bukhu Lophunzitsira
Häftad, Nyanja, 2025
197 kr
Beställningsvara. Skickas inom 7-10 vardagar. Fri frakt över 249 kr.
Beskrivning
Buku la Mamasulidwa a kwa Omangidwa limapereka zinthu zapadera zoperekera machiritso ndi ufulu. Limapereka makiyi ogwiritsira ntchito mphamvu ya mtanda kutenga 'ufulu wa ulemerero wa ana a Mulungu' (Aroma 8:21 ).
Mapemphero ndi zolengeza mu masamba awa zayesedwa m'makontinenti asanu ndi limodzi. Zatsimikizira kuthekera kothandiza kumasula anthu, kuswa linga la mibadwo ndi kuwamasula kukhala mboni zolimba mtima ndi zogwira mtima za mphamvu yopulumutsa ya Khristu.